Loading...

Download
  • Genre:Afrobeats
  • Year of Release:2022

Lyrics

Nghazzie, Ayayaa...


Phalirani Ma Hopu Yane Sono Natora

Chi Type Changa Sure, Chi Shape Chamakora

Koma Bengende, Dairy Bengende

Kutemwa Bengende, Haya Bengende


Wakondali Nde Khalidwe Lanji?

Kundipatsachi Chikondi Chanji?

Tsiku Lonse Mangokhalira Kuvula

Ntchito Yanga Nzikuveka Nde Udindo Wanji?


Magonedwe Ako Myendo Kpachikana

Sungangokhala Umakonda Ksamilana

Kwamakolo Anga Sindngakutengere

Ndiwe Nkazi Wautchisi Umakonda Knyambitana


Kungo Tenthedwa Pang'ono Umati Tivule

Kukangozizira Tsiku Lonse Tifunde

Manja Ako Ali Kakaka Pa Remote

Kuseweretsa,Kugwiragwira Ma Battery


Phalirani Ma Hopu Yane Sono Natora

Chi Type Changa Sure, Chi Shape Chamakora

Koma Bengende, Dairy Bengende

Kutemwa Bengende, Haya Bengende


Mayiwatu Ati Ndsama Chokechoke

Ndkadyaidya Ndsamaka Yendeyende

Ati Pano Nzanga Ndi Iwowo Basi

Nde Pakhomo Pano Alendo Asama Bwerebwere


Kuti Asama Thokethoke Ndekuti Ndzimu Kisaskisa

Kuti Asamayendeyende Neyo Ndzimu Gwilagwila

Nkazi Wanji Ndapezayu? Konda Kugwilagwila Mutu

Chita Ku Chondelela Osama Vulava


Phalirani Ma Hopu Yane Sono Natora

Chi Type Changa Sure, Chi Shape Chamakora

Koma Bengende, Dairy Bengende

Kutemwa Bengende, Haya Bengende


Phalirani Ma Hopu Yane Sono Natora

Chi Type Changa Sure, Chi Shape Chamakora

Koma Bengende, Dairy Bengende

Kutemwa Bengende, Haya Bengende


Kugulugusha Nkazi Konda Gwilagwila

Kunyengerela Nkazi Konda Flasha Flasha

Konda Kpanga Zinthu Nkazi Ktsekemela

Funa Kampeni Kumphasa Nkazi Kchita Knjenjemela


She's Like, Guy Go Down Low Sindnatope

Funa Ndikuchengetele

Am Like, Ok I'll Go Low

Got A Brand New Style Ndikupinde


Ufuna Ndikukwere Ndikupalase, Nditchove Ngati Njinga

All Night Nkazzi Ndiwe Makina

Ufuna Ndiku Tchetchelele Uli Bengende

Mpaka Kuche Ndijombese Ku Ntchito


Phalirani Ma Hopu Yane Sono Natora

Chi Type Changa Sure, Chi Shape Chamakora

Koma Bengende, Dairy Bengende

Kutemwa Bengende, Haya Bengende


Phalirani Ma Hopu Yane Sono Natora

Chi Type Changa Sure, Chi Shape Chamakora

Koma Bengende, Dairy Bengende

Kutemwa Bengende, Haya Bengende

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status