![TDLS (true daily life situations)](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/08/02/11b49acef494405b8d49edd4953f79d2_464_464.jpg)
TDLS (true daily life situations) Lyrics
- Genre:Pop
- Year of Release:2023
Lyrics
TDLS (true daily life situations) - VanOfo
...
eeeh
na na na naaa
van(zosayenda entertainment)
alavya! alavya aah
pachiyambi zinthu zinali bhobo
ndipo sogolo likaoneka
koma after atangomwalira bambo
moyo unayamba kuphweka
posakhalitsa mom anapeza mwamuna
yemwe anatichotsa mumavuto
koma kwaine nagwira Lamoto mfuwa
poti akandigwilira amami akachokapo
paka anandiptsa mimba
plus matenda
akati sanene kwa anthu akandiopseza
tawauza amami nawoso ananditcheza
kuti ndingozitsiya poti akatithandiza
koma inu nkhaza ziliipo eeyah
achinyamata tili mavutooo simasewera
TDLS