![Ukulonjeza](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/08/28/b4426168fabe480fbba9a54943553daf_464_464.jpg)
Ukulonjeza Lyrics
- Genre:Pop
- Year of Release:2023
Lyrics
Ukulonjeza - VanOfo
...
eeeeeeh!
aaaah zosayenda entertainment
(Alavya x2) (I need you eeh)
van(amwenye okuda)
Nadine mphawi koma unalonjeza kuzandikonda paka Manda
Nanga kutabwera mafana ovaya andalamawa eah
Straight kwa makolo ako kukapepa banja
Ukulonjeza kuti iwe uzakharabe kumbali yanga babe?
Iwe umandikonda nanga kwanu atandikana?
Ndikukupezera mwamuna wina tchana
Ukulonjeza kuzakhumudwitsa makolo ako ndikuyimikika kumbali yanga?
say the truth ndikufuna ndiziwiretu
Ngati kuli kusweka mtima uswekeretu
Ngati kuli kulira ine ndililiretu
chifukwa mtima mwangamu
Nde ndumakhara (ndi matha ×3)
ndikakuptsa chikondi changa
iwe suzasinda mawayangaaa?
Ine ndumakhara (ndi matha ×3)
(Ukulonjeza ×8) babe
babe promise that you will never me alone
babe promise that you will never change yourself
babe promise
if you will never leave a alone
babe promise
if you will never change yourself
babe promise
if you will never treat me bad
babe promise
if you will never break my heart
babe promise
if you will never leave me alone
babe promise
if you will never change yourself
babe promise
if you will never treat me bad
babe promise
if you will never break my heart
Ado wanna waist your time
Ado wanna waist my time
just tell me if you really love me
Ado wanna waist your time
A do wanna waist my time
just tell me if you really love me yeh
a wanna let you know, your the shadow of my life
lemmi tell you that, your the one that I love you
I wanna let you know, you the shadow of my life
lemmi tell you that, your the one that I love uuuuh yeh
ndikumakhara (ndi matha ×3)
ndikakupatsa chikondi changa iwe suzasintha mawanga?
ine ndumakhara (ndi matha ×3)
ndikakupatsa chikond changa iwe suzasinda mawanga?
(UKULONJEZA ×8) babe
Sikuti ndiwe oyamba
kundiuza zonsezi ena andiuzapo
Akapempha chikondi changa
Look like innocent koma anandilizapo
Akati ndikawakonda sizalira
pamavuto chanza azandigwira
koma tawakonda akasintha ngati syllabus
anandivura kenako kundisiya basi
ndikumakhara (ndi mantha ×3) mantha ×3
ndikakupatsa chikondi changa,iwe suzasinda mawanga?
ime ndikumakhara (ndi mantha x3)
ndikakupatsa chikondi changa, iwe suzasinda mawanga ?
(UKULONJEZA ×8)
ndikumakhara (ndi mantha ×3) mantha ×3
ndikakupatsa chikondi changa,iwe suzasinda mawanga?
ime ndikumakhara (ndi mantha x3)
ndikakupatsa chikondi changa, iwe suzasinda mawanga ?
(UKULONJEZA ×8)
8